Skip to content

Wanangwa Chafulumira

Organization The Times Group

Pays Malawi

Région Afrique du Sud

Secteur

Poste / titre du poste Editor

map

My experience in adult learning and education

Ndimatsatira nkhani za sukulu za kwacha ndi jambula mapologalamu a kanema mmdera osiyanasiyana. Chimandipatsa chidwi ndi chikhumbokhumbo chimene anthu alinacho kuti adziwe kulemba, kuwerenga ndi kuwrrengera poganizaso kuti amatha kulumikiza gawo lamaphunziro pachitukuko.